Psalms 112:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zidzukulu zake zidzakhala zamphamvu pa dziko lapansi. Ana a munthuyo adzakhala odala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbeu yake idzakhala yamphamvu pa dziko lapansi; mbadwo wa oongoka mtima udzadalitsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana ake adzakhala amphamvu mʼdziko; mʼbado wa olungama mtima udzadalitsidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbeu yace idzakhala yamphamvu pa dziko lapansi; Mbadwo wa oongoka mtima udzadalitsidwa.