Psalms 112:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Banja lake lidzakhala lachuma ndi lolemera, ndipo kulungama kwake kudzakhala kwamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'nyumba mwake mudzakhala akatundu ndi chuma: Ndi chilungamo chake chikhala chikhalire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulemera ndi chuma zili mʼnyumba yake, ndipo chilungamo chake ndi chosatha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'nyumba mwace mudzakhala akatundu ndi cuma: Ndi cilungamo cace cikhala cikhalire.