Psalms 112:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale nthaŵi ya mdima, munthu wochita chilungamo ayenda m'kuŵala, chifukwa ngwokoma mtima, wachifundo ndi woongoka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuunika kutulukira oongoka mtima mumdima; Iye ndiye wachisomo, ndi wansoni ndi wolungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale mu mdima kuwala kumatulukira olungama mtima; wokoma mtima, wachifundo ndi wowongoka mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuupika kuturukira oongoka mtima mumdima; Iye ndiye wacisomo; ndi wansoni ndi wolungama.