Psalms 112:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali wolimba mtima, sadzachita mantha, potsiriza adzaona adani ake atagonja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wake ngwochirikizika, sadzachita mantha, kufikira ataona chofuna iye pa iwo omsautsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wake ndi wotetezedwa, sadzakhala ndi mantha; potsiriza pake adzayangʼana adani ake mwachipambano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wace ngwocirikizika, sadzacita mantha, Kufikira ataona cofuna iye pa iwo omsautsa.