Psalms 112:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapereka chithandizo mwaufulu, amaoloŵa manja kwa anthu osauka. Chilungamo chake chidzakhala chamuyaya, adzakhala wamphamvu ndipo anthu adzampatsa ulemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anagawagawa, anapatsa aumphawi; chilungamo chake chikhalitsa kosatha; nyanga yake idzakwezeka ndi ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wopereka mphatso zake mowolowamanja kwa osauka, chilungamo chake chimanka mpaka muyaya; nyanga yake idzakwezedwa mwaulemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anagawagawa, anapatsa aumphawi; Cilungamo cace cikhalitsa kosatha; Nyanga yace idzakwezeka ndi ulemu.