Psalms 113:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzina la Chauta litamandike kuyambira ku matulukiro a dzuŵa mpaka ku maloŵero ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chitulukire dzuwa kufikira kulowa kwake lilemekezedwe dzina la Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyambira ku matulukiro a dzuwa mpaka ku malowero ake, dzina la Yehova liyenera kutamandidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Citurukire dzuwa kufikira kulowa kwace Lilemekezedwe dzina la Yehova.