Psalms 113:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
wochita kuŵeramira pansi poyang'ana mlengalenga ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadzichepetsa apenye zam'mwamba ndi za pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene amawerama pansi kuyangʼana miyamba ndi dziko lapansi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nadzicepetsa apenye Zam'mwamba ndi za pa dziko lapansi.