Psalms 113:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakweza munthu wosauka kuchokera ku fumbi, ndipo amatulutsa ku dzala anthu osoŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene autsa wosauka kumchotsa kufumbi, nakweza waumphawi kumchotsa kudzala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amakweza munthu wosauka kuchoka pa fumbi ndi kutukula munthu wosowa kuchoka pa dzala;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene autsa wosauka lrumcotsa kupfumbi, Nakweza waumphawi kumcotsa kudzala.