Psalms 113:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaŵakhazika pamodzi ndi mafumu, mafumu a anthu a Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti amkhalitse pamodzi ndi akulu, pamodzi ndi akulu a anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amawakhazika pamodzi ndi mafumu, pamodzi ndi mafumu a anthu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti amkhalitse pamodzi ndi akulu, Pamodzi ndi akulu a anthu ace.