Psalms 113:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapatsa banja mkazi wosabala, namsandutsa mai wosangalala wa ana. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asungitsa nyumba mkazi wosaona mwana, akhale mai wokondwera ndi ana. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amakhazikitsa mayi wosabereka mʼnyumba yake monga mayi wa ana wosangalala. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asungitsa nyumba mkazi wosaonamwana, Akhale mai wokondwera ndi ana. Haleluya.