Psalms 114:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yuda adasanduka malo opatulika a Chauta, Aisraele adasanduka anthu a mu ufumu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yuda anakhala malo ake oyera, Israele ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yuda anasanduka malo opatulika a Mulungu, Israeli anasanduka ufumu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yuda anakhala malo ace oyera, Israyeli ufumu wace.