Psalms 114:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyanja idaona zimenezi nithaŵa, mtsinje wa Yordani udabwerera m'mbuyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyanjayo inaona, nithawa; Yordani anabwerera m'mbuyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyanja inaona ndi kuthawa, mtsinje wa Yorodani unabwerera mʼmbuyo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyanjayo inaona, nithawa; Yordano anabwerera m'mbuyo.