Psalms 114:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mapiri, chikukuvutani nchiyani, kuti muzilumphalumpha ngati nkhosa zamphongo? Nanga inu zitunda, mukulumphiranji ngati anaankhosa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munatumphatumphiranji ngati nkhosa zamphongo, mapiri inu? Ngati anaankhosa, zitunda inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
inu mapiri, munalumphalumphiranji ngati nkhosa zazimuna, inu timapiri, ngati ana ankhosa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munatumpha-tumphiranji ngati nkhosa zamphongo, mapiri inu? Ngati ana a nkhosa, zitunda inu?