Psalms 114:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye amasandutsa thanthwe kukhala dziŵe lamadzi, amasandutsa mwala wolimba kukhala kasupe wa madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene anasanduliza thanthwe likhale thawale lamadzi, nsangalabwi ikhale kasupe wamadzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene anasandutsa thanthwe kukhala chitsime, thanthwe lolimba kukhala akasupe a madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene anasanduliza thanthwe likhale thawale lamadzi, Nsangalabwi ikhale kasupe wamadzi.