Psalms 115:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwa ife ai, Chauta, kwa ife ai, koma kwa dzina lanu lokha ndiye kukhale ulemerero. Chifukwa ndinu Mulungu wa chikondi chosasinthika ndi wokhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa ife ai, Yehova, kwa ife ai, koma kwa dzina lanu patsani ulemerero, chifukwa cha chifundo chanu, ndi choonadi chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa ife ayi Yehova, kwa ife ayi koma ulemerero ukhale pa dzina lanu, chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika ndiponso chifukwa cha kukhulupirika kwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa ife ai, Yehova, kwa ife ai, Koma kwa dzina lanu patsani ulemerero, Cifukwa ca cifundo canu, ndi coonadi canu.