Psalms 115:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta watikumbukira ndipo adzatidalitsa. Adzadalitsa anthu a Israele, adzadalitsa banja la Aroni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova watikumbukira; adzatidalitsa: adzadalitsa nyumba ya Israele; adzadalitsa nyumba ya Aroni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova watikumbukira ndipo adzatidalitsa: adzadalitsa nyumba ya Israeli, adzadalitsa nyumba ya Aaroni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova watikumbukila; adzatidalitsa: Adzadalitsa nyumba ya Israyeli; Adzadalitsa nyumba ya Aroni.