Psalms 115:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akudalitseni Chauta, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Odalitsika inu a kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudalitsidwe ndi Yehova, Wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Odalitsika inu a kwa Yehova, Wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.