Psalms 115:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumwamba nkwa Chauta, koma dziko lapansi adapatsa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za kumwamba, kumwamba ndiko kwa Yehova; koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumwamba ndi kwa Yehova, koma dziko lapansi Iye walipereka kwa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za kumwamba, kumwamba ndiko kwa Yehova; Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.