Psalms 115:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mafano ao ndi asiliva ndi agolide, opangidwa ndi manja a anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafano ao ndiwo a siliva ndi golide, ntchito za manja a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mafano awo ndi siliva ndi golide, opangidwa ndi manja a anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafano ao ndiwo a siliva ndi golidi, Nchito za manja a anthu.