Psalms 115:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakamwa ali napo, koma salankhula. Maso ali nawo, koma sapenya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakamwa ali napo, koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakamwa ali napo koma sayankhula, maso ali nawo koma sapenya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakamwa ali napo, koma osalankhula; Maso ali nao, koma osapenya;