Psalms 115:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manja ali nawo, koma akakhudza, samva kanthu. Miyendo ali nayo, koma sayenda, ndipo satulutsa ndi liwu lomwe kukhosi kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
manja ali nao, koma osagwira; mapazi ali nao, koma osayenda; kapena sanena pammero pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
manja ali nawo koma akakhudza samva kanthu; mapazi ali nawo koma sayenda; kapena pakhosi pawo kutulutsa mawu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Manja ali nao, koma osagwira; Mapazi ali nao, koma osayenda; Kapena sanena pammero pao,