Psalms 115:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene amapanga mafanowo amafanafana nawo, chimodzimodzi onse amene amaŵakhulupirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzafanana nao iwo akuwapanga; ndi onse akuwakhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amene amapanga mafanowo adzafanana nawo, chimodzimodzinso onse amene amadalira mafanowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzafanana nao iwo akuwapanga; Ndi onse akuwakhulupirira,