Psalms 116:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimakonda Chauta chifukwa amamva mau anga omupemba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndimkonda, popeza Yehova amamva mau anga ndi kupemba kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimakonda Yehova pakuti Iyeyo amamva mawu anga; Iye amamva kulira kwanga kopempha chifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndimkonda, popeza Yehova amamva, Mau anga ndi kupemba kwanga.