Psalms 116:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakhulupirirabe ngakhale pamene ndinkati, “Ndazunzika koopsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinakhulupirira, chifukwa chake ndinalankhula; ndinazunzika kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinakhulupirira; choncho ndinati, “Ndasautsidwa kwambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinakhulupirira, cifukwa cace ndinalankhula; Ndinazunzika kwambiri.