Psalms 116:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndinkachita mantha, ndidati, “Anthu ndi osakhulupirika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pofulumizidwa mtima ndinati ine, anthu onse nga mabodza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndili mʼnkhawa yanga ndinati, “Anthu onse ndi abodza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pofulumizidwa mtima ndinati ine, Anthu Onse nga mabodza.