Psalms 116:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, ine ndine mtumiki wanu, mtumiki wanu weniweni, mwana wa mdzakazi wanu. Inu mwamasula maunyolo anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiloleni, Yehova, indetu ndine mtumiki wanu; ndine mtumiki wanu, mwana wa mdzakazi wanu; mwandimasulira zondimanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, zoonadi ndine mtumiki wanu: ndine mtumiki wanu, mwana wa mdzakazi wanu; Inu mwamasula maunyolo anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiloleni, Yehova, indetu ndine mtumiki wanu; Ndine mtumiki wanu, mwana wa mdzakazi wanu; Mwandimasulira zondimanga,