Psalms 116:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye amatchera khutu kuti andimve, nchifukwa chake ndidzampempha nthaŵi zonse pamene ndili moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza amanditcherera khutu lake, chifukwa chake ndidzaitanira Iye masiku anga onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ananditchera khutu, ndidzayitana Iye masiku onse a moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza amandicherera khutu lace, Cifukwa cace ndidzaitanira Iye masiku anga onse.