Psalms 116:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Misampha ya imfa idandizinga, zoopsa za m'dziko la akufa zidandigwera. Ndidaona mavuto, nkugwidwa ndi nthumanzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zingwe za imfa zinandizinga, ndi zowawa za manda zinandigwira: ndinapeza nsautso ndi chisoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zingwe za imfa zinandizinga, zoopsa za ku dziko la anthu akufa zinandigwera; ndinapeza mavuto ndi chisoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zingwe za imfa zinandizinga, Ndi zowawa za manda zinandigwira: Ndinapeza nsautso ndi cisoni.