Psalms 116:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidapemphera potchula dzina la Chauta kuti, “Chauta ndikukupemphani, pulumutsani moyo wanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinaitana dzina la Yehova; ndikuti, Yehova ndikupemphani landitsani moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo ndinayitana dzina la Yehova: “Inu Yehova, pulumutseni!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinaitana dzina la Yehova; Ndikuti, Yehova ndikupemphani landitsani moyo wanga.