Psalms 116:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amasunga a mtima wodzichepetsa. Pamene ndidagwa m'zoopsa, Iye adandipulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova asunga opusa; ndidafooka ine, koma anandipulumutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amateteza munthu wodzichepetsa mtima; pamene ndinali ndi chosowa chachikulu, Iye anandipulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova asunga opusa; Ndidafoka ine, koma anandipulumutsa,