Psalms 116:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe mtima wanga, bwerera ku malo ako opumulira, chifukwa Chauta wakuchitira zokoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ubwere moyo wanga ku mpumulo wako; pakuti Yehova anakuchitira chokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pumula iwe moyo wanga, pakuti Yehova wakuchitira zokoma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ubwere moyo wanga ku mpumulo wako; Pakuti Yehova anakucitira cokoma.