Psalms 116:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Inu Chauta, mwandipulumutsa ku imfa, mwaletsa misozi yanga, mwanditeteza kuti ndisaphunthwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti munalanditsa moyo wanga kuimfa, maso anga kumisozi, mapazi anga, ndingagwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu Yehova mwapulumutsa moyo wanga ku imfa, maso anga ku misozi, mapazi anga kuti angapunthwe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti munalanditsa moyo wanga kuimfa, Maso anga kumisozi, Mapazi anga, ndingagwe.