Psalms 116:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimayenda pamaso pa Chauta m'dziko la amoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzayenda pamaso pa Yehova m'dziko la amoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti ine ndiyende pamaso pa Yehova mʼdziko la anthu amoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzayenda pamaso pa Yehova M'dziko la amoyo.