Psalms 117:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti chikondi chake kwa ife nchachikulu, kukhulupirika kwa Chauta nkwamuyaya. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chifundo chake cha pa ife ndi chachikulu; ndi choonadi cha Yehova nchosatha. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti chikondi chake pa ife ndi chachikulu, ndipo kukhulupirika kwa Yehova nʼkosatha. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cifundo cace ca pa ife ndi cacikuru; Ndi coonadi ca Yehova ncosatha. Haleluya.