Psalms 118:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani a mitundu yonse adandizinga, koma ndidaŵaononga ndi mphamvu za dzina la Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amitundu onse adandizinga, zedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a mitundu yonse anandizinga, koma mʼdzina la Yehova ndinawawononga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amitundu onse adandizinga, Zedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.