Psalms 118:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandizinga ngati njuchi, koma adatha msanga ngati moto wapaminga. Ndidaŵaononga ndi mphamvu za dzina la Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adandizinga ngati njuchi; anazima ngati moto waminga; indedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anandizinga ngati njuchi, koma anatha msanga ngati moto wapaminga; mʼdzina la Yehova ndinawawononga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adandizinga ngati njuci; Anazima ngati moto waminga; Indedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.