Psalms 118:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandikankha kwambiri, kotero kuti ndinali pafupi kugwa, koma Chauta adandithandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kundikankha anandikankha ndikadagwa; koma Yehova anandithandiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anandikankha uku ndi uko ndipo ndinali pafupi kugwa, koma Yehova anandithandiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kundikankha anandikankha ndikadagwa; Koma Yehova anandithandiza.