Psalms 118:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mverani nyimbo m'mahema mwa anthu a Mulungu, nyimbo zokondwerera kupambana, zakuti, “Dzanja lamanja la Chauta limagonjetsa mwamphamvu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mahema a olungama muli liu lakufuula mokondwera Dzanja lamanja la Yehova ndi la chipulumutso:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfuwu wachimwemwe ndi chipambano ukumveka mʼmatenti a anthu olungama mtima kuti: “Dzanja lamanja la Yehova lachita zamphamvu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mahema a olungama muli liu lakupfuula mokondwera ndi la cipulumutso: