Psalms 118:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidzafa, ndidzakhala moyo, ndipo ndidzalalika ntchito za Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo, ndipo ndidzafotokozera ntchito za Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo ndipo ndidzalalika za ntchito ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo, Ndipo ndidzafotokozera nchito za Yehova.