Psalms 118:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwala umene amisiri omanga nyumba adaukana, womwewo wasanduka mwala wapangodya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwala umene omangawo anaukana wakhala mutu wa pangodya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwala umene amisiri omanga nyumba anawukana wasanduka wapangodya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwala umene omangawo anaukana Wakhala mutu wa pangondya.