Psalms 118:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngwodala amene alikudza m'dzina la Chauta. Tikufunirani madalitso ochokera m'nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala wakudzayo m'dzina la Yehova; takudalitsani kochokera m'nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wodala amene akubwera mʼdzina la Yehova. Tikukudalitsani kuchokera ku nyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala wakudzayo m'dzina la Yehova; Takudalitsani kocokera m'nyumba ya Yehova.