Psalms 118:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndi Mulungu, ndipo watipatsa kuŵala. Yambani mdipiti wachikondwerero mutatenga nthambi, mpaka kukafika ku guwa lansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye Mulungu, amene anatiunikira; mangani nsembe ndi zingwe, kunyanga za guwa la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi Mulungu, ndipo kuwala kwake kwatiwunikira Ife. Lowani nawo pa mʼdipiti wa ku chikondwerero mutanyamula nthambi mʼdzanja lanu, mpaka ku nyanga za guwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye Mulungu, amene anatiunikira; Mangani nsembe ndi zingwe, ku nyanga za guwa la nsembe.