Psalms 118:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oopa Chauta anene kuti, “Chikondi chake nchamuyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anene tsono iwo akuopa Yehova, kuti chifundo chake nchosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene amaopa Yehova anene kuti: “Chikondi chake ndi chosatha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anene tsono iwo akuopa Yehova, Kuti cifundo cace ncosatha.