Psalms 118:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ali pa mbali yanga kuti andithandize. Odana nane ndidzaŵayang'ana monyoza nditaŵapambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndi wanga, mwa iwo akundithandiza; m'mwemo ndidzaona chofuna ine pa iwo akundida.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ali nane; Iye ndiye thandizo langa. Ndidzayangʼana adani anga mwachipambano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndi wanga, mwa iwo akundithandiza; M'mwemo ndidzaona cofuna ine pa iwo akundida,