Psalms 118:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuthaŵira kwa Chauta nkwabwino kupambana kukhulupirira munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼkwabwino kuthawira kwa Yehova kusiyana ndi kudalira munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuthawira kwa Yehova nkokoma Koposa kukhulupirira munthu.