Psalms 118:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuthaŵira kwa Chauta nkwabwino kupambana kukhulupirira mafumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira akulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼkwabwino kuthawira kwa Yehova kusiyana ndi kudalira mafumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuthawira kwa Yehova nkokoma Koposa kukhulupirira akulu,