Psalms 119:131 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimapuma mwaŵefuŵefu nditatsekula pakamwa, chifukwa ndimalakalaka malamulo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinatsegula pakamwa panga, ndi kupuma wefuwefu; popeza ndinakhumba malamulo anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimatsekula pakamwa panga ndi kupuma wefuwefu, kufunafuna malamulo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinatsegula pakamwa panga, ndi kupuma wefu wefu; Popeza ndinakhumba malamulo anu.