Psalms 119:157 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ondizunza ndiponso adani anga ngochuluka, koma sindisiyana nawo malamulo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ondilondola ndi ondisautsa ndiwo ambiri; koma sindinapatukana nazo mboni zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani amene akundizunza ndi ambiri, koma ine sindinatembenuke kuchoka pa umboni wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ondilondola ndi ondisautsa ndiwoambiri; Koma sindinapatukana nazo mboni zanu.