Psalms 119:161 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu amandizunza popanda chifukwa, koma mtima wanga umaopa mau anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nduna zinandilondola kopanda chifukwa; koma mtima wanga uchita mantha nao mau anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Olamulira amandizunza popanda chifukwa, koma mtima wanga umanjenjemera ndi mawu anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nduna zinandilondola kopanda cifukwa; Koma mtima wanga ucita mantha nao mau anu.