Psalms 119:61 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale anthu oipa anditchere msampha, sindiiŵala malamulo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandikulunga nazo zingwe za oipa; koma sindinaiwala chilamulo chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale oyipa andimange ndi zingwe, sindidzayiwala lamulo lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandikulunga nazo zingwe za oipa; Koma sindinaiwala cilamulo canu.